Yesaya 43:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tiye tikhale pa mlandu. Ndikumbutse.+ Fotokoza mbali yako kuti iweyo ukhale wosalakwa.+ Yeremiya 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Koma iwe ukuti, ‘Ine ndilibe mlandu uliwonse. Ndithudi mkwiyo wake wandichokera.’+ “Tsopano ndikuyamba kukuimba mlandu chifukwa chonena kuti, ‘Sindinachimwe.’+ Hoseya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani mawu a Yehova inu ana a Isiraeli. Yehova ali ndi mlandu ndi anthu okhala m’dzikoli,+ chifukwa m’dzikoli mulibe choonadi,+ kukoma mtima kosatha, ndiponso anthu a m’dzikoli amachita zinthu ngati kuti sadziwa Mulungu.+
35 “Koma iwe ukuti, ‘Ine ndilibe mlandu uliwonse. Ndithudi mkwiyo wake wandichokera.’+ “Tsopano ndikuyamba kukuimba mlandu chifukwa chonena kuti, ‘Sindinachimwe.’+
4 Tamverani mawu a Yehova inu ana a Isiraeli. Yehova ali ndi mlandu ndi anthu okhala m’dzikoli,+ chifukwa m’dzikoli mulibe choonadi,+ kukoma mtima kosatha, ndiponso anthu a m’dzikoli amachita zinthu ngati kuti sadziwa Mulungu.+