1 Mafumu 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+ Miyambo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yokhulupirika ndi imene sinama,+ koma mboni yonyenga imanena bodza lokhalokha.+ Mika 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita bwino kwambiri.+ Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso, ndipo woweruza amalandira chiphuphu poweruza.+ Munthu wotchuka amangolankhula zolakalaka za mtima wake+ ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu. Machitidwe 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako mwamseri ananyengerera amuna ena kuti anene kuti:+ “Tamumva ife ameneyu akulankhula mawu onyoza+ Mose ndi Mulungu.”
10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+
3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita bwino kwambiri.+ Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso, ndipo woweruza amalandira chiphuphu poweruza.+ Munthu wotchuka amangolankhula zolakalaka za mtima wake+ ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu.
11 Kenako mwamseri ananyengerera amuna ena kuti anene kuti:+ “Tamumva ife ameneyu akulankhula mawu onyoza+ Mose ndi Mulungu.”