Levitiko 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wonyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Khamu lonse lizim’ponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.+ Yohane 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ayudawo anamuyankha kuti: “Sitikukuponya miyala chifukwa cha ntchito yabwino ayi, koma chifukwa chonyoza Mulungu.+ Iwe ndiwe munthu wamba koma ukudziyesa mulungu.”+ Machitidwe 7:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Atamutulutsira kunja kwa mzinda,+ anayamba kumuponya miyala.+ Ndipo mboni+ zinaika malaya awo akunja pafupi ndi mnyamata wina dzina lake Saulo.+
16 Wonyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Khamu lonse lizim’ponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.+
33 Ayudawo anamuyankha kuti: “Sitikukuponya miyala chifukwa cha ntchito yabwino ayi, koma chifukwa chonyoza Mulungu.+ Iwe ndiwe munthu wamba koma ukudziyesa mulungu.”+
58 Atamutulutsira kunja kwa mzinda,+ anayamba kumuponya miyala.+ Ndipo mboni+ zinaika malaya awo akunja pafupi ndi mnyamata wina dzina lake Saulo.+