Salimo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’kamwa mwake mwadzaza matemberero, chinyengo ndi kupondereza ena.+Pansi pa lilime lake pamatuluka mavuto ndi zopweteka ena.+ 2 Petulo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuwonjezera apo, ambiri adzatsatira+ khalidwe lotayirira+ la aphunzitsiwo, ndipo chifukwa cha amenewa, anthu adzalankhula monyoza njira ya choonadi.+
7 M’kamwa mwake mwadzaza matemberero, chinyengo ndi kupondereza ena.+Pansi pa lilime lake pamatuluka mavuto ndi zopweteka ena.+
2 Kuwonjezera apo, ambiri adzatsatira+ khalidwe lotayirira+ la aphunzitsiwo, ndipo chifukwa cha amenewa, anthu adzalankhula monyoza njira ya choonadi.+