1 Mafumu 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+ Machitidwe 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako mwamseri ananyengerera amuna ena kuti anene kuti:+ “Tamumva ife ameneyu akulankhula mawu onyoza+ Mose ndi Mulungu.”
10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+
11 Kenako mwamseri ananyengerera amuna ena kuti anene kuti:+ “Tamumva ife ameneyu akulankhula mawu onyoza+ Mose ndi Mulungu.”