Salimo 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Simunandipereke m’manja mwa adani.+Mwapondetsa phazi langa pamalo otakasuka.+ Salimo 35:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Musalole kuti mumtima mwawo anene kuti: “Eya! Izi ndi zimene timafuna.”+Ndipo asanene kuti: “Tamumeza.”+ Salimo 41:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova adzamuteteza ndi kumusunga ali wamoyo.+Adzatchedwa wodala padziko lapansi.+Ndipo Mulungu sangamupereke kwa adani ake.+ Salimo 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukatero ndidziwa kuti mwasangalala nane,Chifukwa mdani wanga sadzafuula mosangalala kuti wandipambana.+
25 Musalole kuti mumtima mwawo anene kuti: “Eya! Izi ndi zimene timafuna.”+Ndipo asanene kuti: “Tamumeza.”+
2 Yehova adzamuteteza ndi kumusunga ali wamoyo.+Adzatchedwa wodala padziko lapansi.+Ndipo Mulungu sangamupereke kwa adani ake.+
11 Mukatero ndidziwa kuti mwasangalala nane,Chifukwa mdani wanga sadzafuula mosangalala kuti wandipambana.+