Salimo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikaitana, mundiyankhe inu Mulungu wanga wolungama.+M’masautso anga mundiimiritse pamalo otakasuka.Mundikomere mtima+ ndipo imvani pemphero langa. Salimo 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ananditenga ndi kundiika pamalo otakasuka.+Anandipulumutsa chifukwa anakondwera nane.+
4 Ndikaitana, mundiyankhe inu Mulungu wanga wolungama.+M’masautso anga mundiimiritse pamalo otakasuka.Mundikomere mtima+ ndipo imvani pemphero langa.