Salimo 149:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Yehova amasangalala ndi anthu ake.+Iye amakongoletsa anthu ofatsa ndi chipulumutso.+