Salimo 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Simunandipereke m’manja mwa adani.+Mwapondetsa phazi langa pamalo otakasuka.+ Salimo 124:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova atamandike, chifukwa sanatipereke kwa iwo+Kuti atikhadzule ngati nyama.+ Yeremiya 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Imbirani Yehova anthu inu! Tamandani Yehova! Pakuti walanditsa moyo wa munthu wosauka m’manja mwa anthu ochita zoipa.+
13 Imbirani Yehova anthu inu! Tamandani Yehova! Pakuti walanditsa moyo wa munthu wosauka m’manja mwa anthu ochita zoipa.+