1 Samueli 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano musalole kuti magazi anga akhetsedwe pamaso pa Yehova,+ pakuti mfumu ya Isiraeli yapita kukasakasaka nthata imodzi,+ monga munthu wothamangitsa nkhwali imodzi m’mapiri.”+ Salimo 118:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munandikankha kwambiri kuti ndigwe,+Koma Yehova anandithandiza.+
20 Tsopano musalole kuti magazi anga akhetsedwe pamaso pa Yehova,+ pakuti mfumu ya Isiraeli yapita kukasakasaka nthata imodzi,+ monga munthu wothamangitsa nkhwali imodzi m’mapiri.”+