Salimo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musandipereke kwa adani anga.+Pakuti mboni zonama zandiukira,+Chimodzimodzinso munthu wachiwawa.+ Salimo 41:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova adzamuteteza ndi kumusunga ali wamoyo.+Adzatchedwa wodala padziko lapansi.+Ndipo Mulungu sangamupereke kwa adani ake.+ Salimo 56:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Ndikomereni mtima inu Mulungu wanga, chifukwa munthu wopanda pake akufuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+Akulimbana nane tsiku lonse ndi kundipondereza.+
2 Yehova adzamuteteza ndi kumusunga ali wamoyo.+Adzatchedwa wodala padziko lapansi.+Ndipo Mulungu sangamupereke kwa adani ake.+
56 Ndikomereni mtima inu Mulungu wanga, chifukwa munthu wopanda pake akufuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+Akulimbana nane tsiku lonse ndi kundipondereza.+