Salimo 57:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba ndi kundipulumutsa.+Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+ [Seʹlah.]Mulungu adzasonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndi choonadi chake.+ Salimo 124:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova akanapanda kukhala kumbali yathu,+Pamene anthu anatiukira,+
3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba ndi kundipulumutsa.+Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+ [Seʹlah.]Mulungu adzasonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndi choonadi chake.+