Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.

  • Salimo 34:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tetezani lilime lanu ku zinthu zoipa,+

      Ndi milomo yanu kuti isalankhule chinyengo.+

  • Salimo 101:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Aliyense wonenera mnzake miseche,+

      Ndimamukhalitsa chete.+

      Sindingathe kupirira zochita za+

      Aliyense wodzikweza ndi wamtima wonyada.+

  • Miyambo 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Amene amayendayenda n’kumanenera ena zoipa+ amaulula zinsinsi za anzake,+ koma wokhulupirika* amabisa nkhani.+

  • Miyambo 20:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Woyenda uku ndi uku n’kumanena zoipa za anthu ena amaulula zinsinsi,+ ndipo usamagwirizane ndi munthu wotengeka ndi milomo yake.+

  • Miyambo 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usanenere wantchito zoipa kwa mbuye wake,+ kuti angakutemberere ndiponso kuti ungakhale ndi mlandu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena