Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova. Miyambo 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amene amayendayenda n’kumanenera ena zoipa+ amaulula zinsinsi za anzake,+ koma wokhulupirika* amabisa nkhani.+ Miyambo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kambirana mlandu wako ndi mnzako,+ ndipo usaulule chinsinsi cha munthu wina,+ Miyambo 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mphepo yochokera kumpoto imabweretsa mvula yambiri. Imakhala ngati kuti yabereka mvulayo ndi ululu wa pobereka.+ Chotero munthu wa lilime loulula chinsinsi amakhala ndi nkhope yonyozedwa.+
16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.
13 Amene amayendayenda n’kumanenera ena zoipa+ amaulula zinsinsi za anzake,+ koma wokhulupirika* amabisa nkhani.+
23 Mphepo yochokera kumpoto imabweretsa mvula yambiri. Imakhala ngati kuti yabereka mvulayo ndi ululu wa pobereka.+ Chotero munthu wa lilime loulula chinsinsi amakhala ndi nkhope yonyozedwa.+