Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 6:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Zitatero, mfumu inalamula kuti abweretse amuna amphamvu amene ananenera Danieli zoipa aja,+ ndipo anawabweretsadi. Kenako anawaponya m’dzenje la mikango+ pamodzi ndi ana awo ndi akazi awo.+ Iwo asanafike n’komwe pansi pa dzenjelo, mikango inawakhadzulakhadzula ndi kuphwanya mafupa awo onse.+

  • Maliko 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 choncho Afarisi ndi alembi amenewa anam’funsa iye kuti: “N’chifukwa chiyani ophunzira anu satsatira miyambo ya makolo, koma amadya chakudya ndi manja oipitsidwa?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena