Luka 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso Yakobo ndi Yohane, ana a Zebedayo,+ amene anali kugwirizana ndi Simoni anadabwa kwambiri. Koma Yesu anauza Simoni kuti: “Usachite mantha. Kuyambira lero uzisodza anthu amoyo.”+
10 Komanso Yakobo ndi Yohane, ana a Zebedayo,+ amene anali kugwirizana ndi Simoni anadabwa kwambiri. Koma Yesu anauza Simoni kuti: “Usachite mantha. Kuyambira lero uzisodza anthu amoyo.”+