Mateyu 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atapitirira pamenepo, anaona amuna enanso awiri+ apachibale, Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane. Iwo anali m’ngalawa limodzi ndi bambo awo, a Zebedayo,+ akusoka maukonde awo, ndipo anawaitana. Maliko 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atapita patsogolo pang’ono, anaona Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane, ali mu ngalawa yawo akusoka maukonde awo.+
21 Atapitirira pamenepo, anaona amuna enanso awiri+ apachibale, Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane. Iwo anali m’ngalawa limodzi ndi bambo awo, a Zebedayo,+ akusoka maukonde awo, ndipo anawaitana.
19 Atapita patsogolo pang’ono, anaona Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane, ali mu ngalawa yawo akusoka maukonde awo.+