Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mayina a atumwi 12+ aja ndi awa:+ Simoni, wotchedwa Petulo,*+ ndi Andireya+ m’bale wake. Yakobo mwana wa Zebedayo+ ndi m’bale wake Yohane.

  • Mateyu 27:56
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 56 Pakati pawo panali Mariya Mmagadala, Mariya mayi a Yakobo ndi Yose, ndiponso panali mayi a Yakobo ndi Yohane.*+

  • Maliko 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Yakobo mwana wa Zebedayo, Yohane m’bale wa Yakobo+ (awiriwa anawatchanso a Boanege, kutanthauza Ana a Bingu),

  • Maliko 10:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Koma Yakobo ndi Yohane, ana aamuna awiri a Zebedayo,+ anapita kwa iye ndi kumuuza kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutichitire chimene tikupempheni.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena