Yohane 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako iye anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyang’ana+ anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane,+ udzatchedwa Kefa” (dzina limene kumasulira kwake ndi Petulo).+ Machitidwe 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+
42 Kenako iye anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyang’ana+ anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane,+ udzatchedwa Kefa” (dzina limene kumasulira kwake ndi Petulo).+
14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+