Maliko 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya* Yesu anaona Simoni+ ndi Andireya m’bale wake wa Simoni, akuponya maukonde awo m’nyanjamo, pakuti anali asodzi.+ Yohane 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Andireya+ m’bale wake wa Simoni Petulo, anali mmodzi wa awiriwo amene anamva zimene Yohane ananena ndi kutsatira Yesu.
16 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya* Yesu anaona Simoni+ ndi Andireya m’bale wake wa Simoni, akuponya maukonde awo m’nyanjamo, pakuti anali asodzi.+
40 Andireya+ m’bale wake wa Simoni Petulo, anali mmodzi wa awiriwo amene anamva zimene Yohane ananena ndi kutsatira Yesu.