Mateyu 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona amuna awiri apachibale akuponya ukonde wophera nsomba m’nyanja, pakuti anali asodzi. Mayina awo anali Simoni+ wotchedwa Petulo+ ndi Andireya. Luka 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atamaliza kulankhula, anauza Simoni kuti: “Palasira kwakuya, ndipo muponye maukonde+ anu kuti muphe nsomba.”
18 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona amuna awiri apachibale akuponya ukonde wophera nsomba m’nyanja, pakuti anali asodzi. Mayina awo anali Simoni+ wotchedwa Petulo+ ndi Andireya.
4 Atamaliza kulankhula, anauza Simoni kuti: “Palasira kwakuya, ndipo muponye maukonde+ anu kuti muphe nsomba.”