Maliko 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho m’gulu la anthu 12 amene anasankha aja munali Simoni, amene anamutchanso Petulo,+ Luka 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kutacha, anaitana ophunzira ake ndi kusankha 12 pakati pawo. Amenewa anawatcha “atumwi.”+ Machitidwe 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atafika mumzindawo anakwera m’chipinda cham’mwamba,+ mmene anali kukhala. Mmenemo munali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wachangu uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+
13 Atafika mumzindawo anakwera m’chipinda cham’mwamba,+ mmene anali kukhala. Mmenemo munali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wachangu uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+