Mateyu 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mayina a atumwi 12+ aja ndi awa:+ Simoni, wotchedwa Petulo,*+ ndi Andireya+ m’bale wake. Yakobo mwana wa Zebedayo+ ndi m’bale wake Yohane. Maliko 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho m’gulu la anthu 12 amene anasankha aja munali Simoni, amene anamutchanso Petulo,+
2 Mayina a atumwi 12+ aja ndi awa:+ Simoni, wotchedwa Petulo,*+ ndi Andireya+ m’bale wake. Yakobo mwana wa Zebedayo+ ndi m’bale wake Yohane.