Maliko 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno anasankha gulu la anthu 12, amenenso anawatcha “atumwi,” kuti azikhala naye nthawi zonse ndi kuti aziwatuma kukalalikira+ Yohane 6:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndinakusankhani inu 12,+ si choncho kodi? Komatu mmodzi wa inu ndi wonenera anzake zoipa.”+
14 Ndiyeno anasankha gulu la anthu 12, amenenso anawatcha “atumwi,” kuti azikhala naye nthawi zonse ndi kuti aziwatuma kukalalikira+
70 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndinakusankhani inu 12,+ si choncho kodi? Komatu mmodzi wa inu ndi wonenera anzake zoipa.”+