Salimo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti m’kamwa mwawo simutuluka mawu okhulupirika.+Mitima yawo yadzaza ndi zinthu zoipa.+Mmero wawo ndi manda otseguka.+Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.+ Maliko 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako anafotokozanso kuti: “Chotuluka mwa munthu n’chimene chimaipitsa munthu.+ Aroma 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Mmero wawo ndi manda otseguka. Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.”+ “M’milomo yawo muli poizoni wa njoka.”+
9 Pakuti m’kamwa mwawo simutuluka mawu okhulupirika.+Mitima yawo yadzaza ndi zinthu zoipa.+Mmero wawo ndi manda otseguka.+Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.+
13 “Mmero wawo ndi manda otseguka. Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.”+ “M’milomo yawo muli poizoni wa njoka.”+