Salimo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalankhulana zabodza.+Amalankhulana ndi milomo yoshashalika+ komanso ndi mitima iwiri.+ Salimo 52:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lilime lako limakonza chiwembu, ndipo ndi lakuthwa ngati lezala,+Limachita zachinyengo.+