Salimo 109:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu woipa ndiponso munthu wachinyengo andinenera zoipa ndi pakamwa pawo.+Iwo anena za ine ndi lilime lonama.+ 2 Akorinto 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti amuna oterowo ndi atumwi onama, antchito achinyengo,+ odzisandutsa atumwi a Khristu.+
2 Munthu woipa ndiponso munthu wachinyengo andinenera zoipa ndi pakamwa pawo.+Iwo anena za ine ndi lilime lonama.+ 2 Akorinto 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti amuna oterowo ndi atumwi onama, antchito achinyengo,+ odzisandutsa atumwi a Khristu.+