2 Samueli 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Abisalomu anali kumuuza kuti: “Taona, nkhani yakoyi ili bwino ndipo ndi yosavuta. Koma mfumu ilibe aliyense woti amvetsere nkhani yakoyi.”+ Salimo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Milomo yachinyengo isowe chonena,+Milomo imene ikulankhula motsutsana ndi wolungama,+ yosadziletsa pa kudzikweza ndi kunyoza ena.+ Miyambo 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mtima wa munthu wolungama umayamba waganiza usanayankhe,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamasefukira zoipa.+ Mateyu 26:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Pa nthawiyi ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda* anali kufunafuna umboni wonama kuti amunamizire mlandu Yesu ndi kumupha+
3 Pamenepo Abisalomu anali kumuuza kuti: “Taona, nkhani yakoyi ili bwino ndipo ndi yosavuta. Koma mfumu ilibe aliyense woti amvetsere nkhani yakoyi.”+
18 Milomo yachinyengo isowe chonena,+Milomo imene ikulankhula motsutsana ndi wolungama,+ yosadziletsa pa kudzikweza ndi kunyoza ena.+
28 Mtima wa munthu wolungama umayamba waganiza usanayankhe,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamasefukira zoipa.+
59 Pa nthawiyi ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda* anali kufunafuna umboni wonama kuti amunamizire mlandu Yesu ndi kumupha+