Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Iwo amalankhulana zabodza.+

      Amalankhulana ndi milomo yoshashalika+ komanso ndi mitima iwiri.+

  • Miyambo 30:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Diso limene limanyoza bambo ake ndiponso limene silimvera mayi ake,+ akhwangwala a kuchigwa* adzalikolowola ndipo ana a chiwombankhanga adzalidya.

  • Mateyu 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mwachitsanzo, Mulungu ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’+ Komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+

  • 2 Petulo 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 koma makamaka anthu amene amafunafuna kugonana ndi anthu ena n’cholinga choti awaipitse,+ ndiponso amene amanyoza owalamulira.+

      Anthu amenewa ndi opanda mantha ndiponso ndi omva zawo zokha, ndipo sanjenjemera ndi anthu aulemerero. M’malomwake, amalankhula zinthu zowanyoza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena