Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Munthu akatemberera bambo ndi mayi ake,+ aziphedwa ndithu.+ Iye watemberera bambo ndi mayi ake. Mlandu wa magazi ake ukhale wa iye mwini.+

  • Deuteronomo 21:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pamenepo amuna onse a mumzinda wawo azim’ponya miyala ndi kumupha. Muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha kwambiri.+

  • 2 Samueli 17:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ndilole chonde, ndisankhe amuna 12,000 kuti ndithamangitse Davide lero usiku.+

  • Miyambo 20:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Aliyense wotemberera bambo ake ndi mayi ake,+ nyale yake idzazimitsidwa kukagwa mdima.+

  • Miyambo 23:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mvera bambo ako amene anakubereka,+ ndipo usanyoze mayi ako chifukwa chakuti akalamba.+

  • Aroma 1:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 ndi miseche.+ Anakhala odana ndi Mulungu, achipongwe,+ odzikweza,+ odzimva,+ oyambitsa zoipa,+ osamvera makolo,+

  • 2 Timoteyo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti anthu adzakhala odzikonda, okonda ndalama, odzimva, odzikweza, onyoza, osamvera makolo,+ osayamika, osakhulupirika,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena