Miyambo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja okhetsa magazi a anthu osalakwa,+ Miyambo 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Lilime lonama limadana ndi amene lam’pweteka,+ ndipo pakamwa polankhula zabwino mokokomeza pamabweretsa chiwonongeko.+ Yeremiya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo amakunga lilime lawo ngati uta kuti aponye chinyengo,+ koma iwo si okhulupirika m’dzikoli. “Iwo anali kuchita zoipa motsatizanatsatizana ndipo anandinyalanyaza,”+ watero Yehova.
28 Lilime lonama limadana ndi amene lam’pweteka,+ ndipo pakamwa polankhula zabwino mokokomeza pamabweretsa chiwonongeko.+
3 Iwo amakunga lilime lawo ngati uta kuti aponye chinyengo,+ koma iwo si okhulupirika m’dzikoli. “Iwo anali kuchita zoipa motsatizanatsatizana ndipo anandinyalanyaza,”+ watero Yehova.