Mateyu 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma zotuluka m’kamwa zimachokera mumtima, ndipo zimenezo zimaipitsa munthu.+