Salimo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti m’kamwa mwawo simutuluka mawu okhulupirika.+Mitima yawo yadzaza ndi zinthu zoipa.+Mmero wawo ndi manda otseguka.+Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.+ Salimo 52:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lilime lako limakonza chiwembu, ndipo ndi lakuthwa ngati lezala,+Limachita zachinyengo.+
9 Pakuti m’kamwa mwawo simutuluka mawu okhulupirika.+Mitima yawo yadzaza ndi zinthu zoipa.+Mmero wawo ndi manda otseguka.+Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.+