Miyambo 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwamuna wamphamvu amene amanena zabwino za mnzake mokokomeza,+ akuyalira ukonde mapazi ake.+ 1 Atesalonika 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipotu, sitinayambe talankhulapo mawu okuyamikirani mwachinyengo,+ (monga mukudziwira), kapena kuchita zachiphamaso+ chifukwa cha kusirira kwa nsanje.+ Mulungu ndiye mboni yathu. Yakobo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chimodzimodzinso lilime. Lilime ndi kachiwalo kakang’ono, koma limadzitama kwambiri.+ Tangoganizani mmene kamoto kakang’onong’ono kamayatsira nkhalango yaikulu.
5 Ndipotu, sitinayambe talankhulapo mawu okuyamikirani mwachinyengo,+ (monga mukudziwira), kapena kuchita zachiphamaso+ chifukwa cha kusirira kwa nsanje.+ Mulungu ndiye mboni yathu.
5 N’chimodzimodzinso lilime. Lilime ndi kachiwalo kakang’ono, koma limadzitama kwambiri.+ Tangoganizani mmene kamoto kakang’onong’ono kamayatsira nkhalango yaikulu.