-
Yakobo 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Lilime nalonso ndi kachiwalo kakangʼono, koma limadzitama kwambiri. Taganizirani mmene kamoto kakangʼono kamayatsira nkhalango yaikulu.
-