Yakobo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chimodzimodzinso lilime. Lilime ndi kachiwalo kakang’ono, koma limadzitama kwambiri.+ Tangoganizani mmene kamoto kakang’onong’ono kamayatsira nkhalango yaikulu. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,12/15/2015, tsa. 1811/15/1997, tsa. 1612/15/1995, tsa. 1910/1/1993, tsa. 32
5 N’chimodzimodzinso lilime. Lilime ndi kachiwalo kakang’ono, koma limadzitama kwambiri.+ Tangoganizani mmene kamoto kakang’onong’ono kamayatsira nkhalango yaikulu.