-
Tito 2:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Nawonso akazi achikulire akhale ndi khalidwe loyenera anthu opembedza. Asakhale amiseche, kapena akapolo a vinyo wambiri, koma akhale aphunzitsi a zinthu zabwino,
-