Genesis 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo, Yehova anaona kuti kuipa kwa anthu kwachuluka padziko lapansi, ndipo malingaliro+ onse a m’mitima ya anthu anali oipa okhaokha nthawi zonse.+ Aroma 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe monga mfumu+ m’matupi anu okhoza kufawo kuti muzitsatira zilakolako zawo.+
5 Pamenepo, Yehova anaona kuti kuipa kwa anthu kwachuluka padziko lapansi, ndipo malingaliro+ onse a m’mitima ya anthu anali oipa okhaokha nthawi zonse.+
12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe monga mfumu+ m’matupi anu okhoza kufawo kuti muzitsatira zilakolako zawo.+