Yesaya 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “‘Adzabwerera kudzera njira imene anadutsa pobwera, ndipo sadzalowa mumzinda uno,’ ndiwo mawu a Yehova.+
34 “‘Adzabwerera kudzera njira imene anadutsa pobwera, ndipo sadzalowa mumzinda uno,’ ndiwo mawu a Yehova.+