2 Mafumu 19:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Adzabwerera kudzera njira imene anadutsa pobwera, ndipo sadzalowa mumzinda uno, ndiwo mawu a Yehova.+ Miyambo 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+
33 Adzabwerera kudzera njira imene anadutsa pobwera, ndipo sadzalowa mumzinda uno, ndiwo mawu a Yehova.+