Salimo 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 N’chifukwa chiyani woipa amanyoza Mulungu?+Mumtima mwake amati: “Simudzandiimba mlandu.”+ Salimo 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+ Yesaya 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi nkhwangwa ingadzikuze kuposa munthu amene akuigwiritsa ntchito? Kapena kodi chochekera matabwa chingadzikweze kuposa munthu amene akuchigwiritsa ntchito? Kodi chikwapu chinganyamule munthu amene wachinyamula m’mwamba, ndiponso kodi ndodo inganyamule m’mwamba munthu amene si mtengo?+
6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+
15 Kodi nkhwangwa ingadzikuze kuposa munthu amene akuigwiritsa ntchito? Kapena kodi chochekera matabwa chingadzikweze kuposa munthu amene akuchigwiritsa ntchito? Kodi chikwapu chinganyamule munthu amene wachinyamula m’mwamba, ndiponso kodi ndodo inganyamule m’mwamba munthu amene si mtengo?+