Ekisodo 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho madziwo anabwereradi,+ ndipo anamiza magaleta ankhondo ndi asilikali apamahatchi a magulu onse ankhondo a Farao, amene analondola Aisiraeli m’nyanjamo.+ Palibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+ Salimo 76:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Hatchi komanso wokwera galeta agona tulo tofa nato chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Mulungu wa Yakobo.+ Ezekieli 39:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Inu mudzakhuta patebulo langa. Mudzadya nyama ya mahatchi, ya okwera magaleta, ya anthu amphamvu ndi ankhondo a mitundu yosiyanasiyana,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+
28 Choncho madziwo anabwereradi,+ ndipo anamiza magaleta ankhondo ndi asilikali apamahatchi a magulu onse ankhondo a Farao, amene analondola Aisiraeli m’nyanjamo.+ Palibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+
6 Hatchi komanso wokwera galeta agona tulo tofa nato chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Mulungu wa Yakobo.+
20 “‘Inu mudzakhuta patebulo langa. Mudzadya nyama ya mahatchi, ya okwera magaleta, ya anthu amphamvu ndi ankhondo a mitundu yosiyanasiyana,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+