Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mwapemerera mpweya wanu,+ ndipo nyanja yawamiza.+

      Amira ngati mtovu m’madzi akuya.+

  • Deuteronomo 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Amenenso sanaone zimene Mulungu anachitira gulu lankhondo la Aiguputo, mahatchi* ake ndi magaleta* ake ankhondo, amene anawamiza m’madzi a m’Nyanja Yofiira pamene anali kukuthamangitsani,+ ndipo Yehova anawononga Iguputo moti ndi mmene zilili kufikira lero.+

  • Nehemiya 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munagawa nyanja+ pamaso pawo ndipo iwo anadutsa panthaka youma pakati pa nyanja.+ Anthu amene anali kuwathamangitsa munawaponya m’nyanja yozama+ ngati mwala+ woponyedwa m’madzi amphamvu.+

  • Salimo 78:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Anapitiriza kuwatsogolera ndi kuwateteza ndipo iwo sanachite mantha.+

      Nyanja inamiza adani awo.+

  • Aheberi 11:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena