Ekisodo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+ Salimo 106:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno madzi anamiza adani awo,+Moti panalibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+ Salimo 136:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amenenso anakutumulira Farao ndi gulu lake lankhondo m’Nyanja Yofiira:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+
15 Amenenso anakutumulira Farao ndi gulu lake lankhondo m’Nyanja Yofiira:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+