Genesis 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wochuluka.+ Ekisodo 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo Aiguputo anawalondola, ndipo mahatchi onse a Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi, anayamba kuwathamangira,+ kulowa pakati pa nyanja. Yoswa 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo, iwo anayamba kufuulira Yehova.+ Choncho ine ndinaika mdima pakati pa iwo ndi Aiguputuwo,+ ndipo ine ndinawamiza ndi madzi a m’nyanja.+ Munaona ndi maso anu zimene ndinachita ku Iguputo.+ Kenako, inu munakhala m’chipululu masiku ambiri.+
14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wochuluka.+
23 Pamenepo Aiguputo anawalondola, ndipo mahatchi onse a Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi, anayamba kuwathamangira,+ kulowa pakati pa nyanja.
7 Pamenepo, iwo anayamba kufuulira Yehova.+ Choncho ine ndinaika mdima pakati pa iwo ndi Aiguputuwo,+ ndipo ine ndinawamiza ndi madzi a m’nyanja.+ Munaona ndi maso anu zimene ndinachita ku Iguputo.+ Kenako, inu munakhala m’chipululu masiku ambiri.+