Ekisodo 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mtambowo unaima pakati pa Aiguputo ndi Aisiraeli.+ Mbali imodzi unali kuchititsa mdima, ndipo mbali ina unali kuwaunikira usiku.+ Ndipo gulu la Aiguputo silinayandikire gulu la Aisiraeli usiku wonse. Salimo 78:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+ Salimo 105:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mulungu anayala mtambo kuti uziwatchinga,+Ndipo anawapatsa moto kuti uziwaunikira usiku.+
20 Mtambowo unaima pakati pa Aiguputo ndi Aisiraeli.+ Mbali imodzi unali kuchititsa mdima, ndipo mbali ina unali kuwaunikira usiku.+ Ndipo gulu la Aiguputo silinayandikire gulu la Aisiraeli usiku wonse.
14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+