2 Timoteyo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 N’chifukwa chake ndikuvutika chonchi,+ koma sindikuchita manyazi.+ Pakuti ndikudziwa amene ndikumukhulupirira, ndipo ndikukhulupirira kuti adzasunga+ chimene ndachiika m’manja mwake kufikira tsikulo.+ 1 Petulo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+
12 N’chifukwa chake ndikuvutika chonchi,+ koma sindikuchita manyazi.+ Pakuti ndikudziwa amene ndikumukhulupirira, ndipo ndikukhulupirira kuti adzasunga+ chimene ndachiika m’manja mwake kufikira tsikulo.+
19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+