Machitidwe 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti ndidzamuonetsa bwinobwino zopweteka zonse zimene ayenera kumva chifukwa cha dzina langa.”+ Aefeso 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa chifukwa chimenechi, ine Paulo, ndine wandende+ mwa Khristu Yesu m’malo mwa inu, anthu a mitundu ina+ . . . 1 Petulo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+
3 Pa chifukwa chimenechi, ine Paulo, ndine wandende+ mwa Khristu Yesu m’malo mwa inu, anthu a mitundu ina+ . . .
19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+