Salimo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma inu mumaona mavuto ndi masautso. Mumayangʼana nʼkuchitapo kanthu.+ Munthu wovutika amayangʼana kwa inu,+ Mumathandiza mwana wamasiye.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:14 Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, tsa. 289
14 Koma inu mumaona mavuto ndi masautso. Mumayangʼana nʼkuchitapo kanthu.+ Munthu wovutika amayangʼana kwa inu,+ Mumathandiza mwana wamasiye.+