Salimo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu mwaona mavuto ndi masautso.Mumawayang’anabe kuti muchitepo kanthu.+Waumphawi,+ mwana wamasiye,* amadziikiza m’manja mwanu.Inu mwakhala mthandizi wake.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:14 Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, tsa. 289
14 Inu mwaona mavuto ndi masautso.Mumawayang’anabe kuti muchitepo kanthu.+Waumphawi,+ mwana wamasiye,* amadziikiza m’manja mwanu.Inu mwakhala mthandizi wake.+